Mateyu 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pakuti kulikonse kumene awiri kapena atatu asonkhana m’dzina langa,+ ine ndidzakhala pakati pawo.”+ Machitidwe 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 chifukwa ine ndili nawe.+ Palibe munthu amene adzakukhudze ndi kukuvulaza, pakuti ndili ndi anthu ambiri mumzinda uno.”
20 Pakuti kulikonse kumene awiri kapena atatu asonkhana m’dzina langa,+ ine ndidzakhala pakati pawo.”+
10 chifukwa ine ndili nawe.+ Palibe munthu amene adzakukhudze ndi kukuvulaza, pakuti ndili ndi anthu ambiri mumzinda uno.”