Mateyu 13:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 ndipo mdani amene anafesa namsongole ndi Mdyerekezi.+ Nthawi yokolola+ ikuimira mapeto a nthawi* ino,+ ndipo okololawo ndi angelo. Mateyu 13:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndi mmenenso zidzakhalire pa mapeto a nthawi* ino: Angelo adzapita n’kukachotsa oipa+ pakati pa olungama+ Mateyu 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atakhala pansi m’phiri la Maolivi, ophunzira anafika kwa iye mwamseri ndi kunena kuti: “Tiuzeni, Kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro cha kukhalapo* kwanu+ ndi cha mapeto a nthawi* ino chidzakhala chiyani?”+
39 ndipo mdani amene anafesa namsongole ndi Mdyerekezi.+ Nthawi yokolola+ ikuimira mapeto a nthawi* ino,+ ndipo okololawo ndi angelo.
49 Ndi mmenenso zidzakhalire pa mapeto a nthawi* ino: Angelo adzapita n’kukachotsa oipa+ pakati pa olungama+
3 Atakhala pansi m’phiri la Maolivi, ophunzira anafika kwa iye mwamseri ndi kunena kuti: “Tiuzeni, Kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro cha kukhalapo* kwanu+ ndi cha mapeto a nthawi* ino chidzakhala chiyani?”+