-
Machitidwe 5:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndiponso anthu ambirimbiri ochokera m’mizinda yozungulira Yerusalemu anali kukhamukira kumeneko, atanyamula anthu odwala komanso amene mizimu yonyansa inali kuwazunza. Ndipo onsewo anali kuchiritsidwa.
-