Mateyu 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Komanso, ngati m’bale wako wachimwa, upite kukam’fotokozera cholakwacho panokha iwe ndi iyeyo.+ Ngati wakumvera, ndiye kuti wabweza m’bale wakoyo.+ 1 Petulo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 koma aleke zoipa+ ndipo achite zabwino. Ayesetse kupeza mtendere ndi kuusunga.+
15 “Komanso, ngati m’bale wako wachimwa, upite kukam’fotokozera cholakwacho panokha iwe ndi iyeyo.+ Ngati wakumvera, ndiye kuti wabweza m’bale wakoyo.+