Mateyu 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero ngati dzanja lako kapena phazi lako limakupunthwitsa, ulidule ndi kulitaya kutali.+ Ndi bwino kuti ukapeze moyo ulibe chiwalo chimodzi kapena uli wolumala kusiyana ndi kuti ukaponyedwe m’moto wosatha uli ndi manja onse awiri kapena mapazi onse awiri.+ Luka 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nyale ya thupi ndi diso lako. Ngati diso lako lili lolunjika pa chinthu chimodzi, thupi lako lonse limawala kwambiri.+ Koma ngati lili loipa, thupi lako limachita mdima.
8 Chotero ngati dzanja lako kapena phazi lako limakupunthwitsa, ulidule ndi kulitaya kutali.+ Ndi bwino kuti ukapeze moyo ulibe chiwalo chimodzi kapena uli wolumala kusiyana ndi kuti ukaponyedwe m’moto wosatha uli ndi manja onse awiri kapena mapazi onse awiri.+
34 Nyale ya thupi ndi diso lako. Ngati diso lako lili lolunjika pa chinthu chimodzi, thupi lako lonse limawala kwambiri.+ Koma ngati lili loipa, thupi lako limachita mdima.