Levitiko 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza khamu lonse la ana a Isiraeli kuti, ‘Mukhale oyera,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wanu ndine woyera.+ Deuteronomo 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ukhale wopanda cholakwa pamaso pa Yehova Mulungu wako.+ Luka 6:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pitirizani kukhala achifundo, potengera Atate wanu amenenso ali wachifundo.+ 1 Petulo 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 chifukwa Malemba amati: “Mukhale oyera, chifukwa ine ndine woyera.”+
2 “Uza khamu lonse la ana a Isiraeli kuti, ‘Mukhale oyera,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wanu ndine woyera.+