2 Mafumu 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma anthu a m’dzikolo anapha anthu onse amene anachitira chiwembu+ Mfumu Amoni. Kenako anthu a m’dzikolo anaika Yosiya+ mwana wake kuti akhale mfumu m’malo mwake. 1 Mbiri 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Manase anabereka Amoni,+ ndipo Amoni anabereka Yosiya.+
24 Koma anthu a m’dzikolo anapha anthu onse amene anachitira chiwembu+ Mfumu Amoni. Kenako anthu a m’dzikolo anaika Yosiya+ mwana wake kuti akhale mfumu m’malo mwake.