Mateyu 18:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo mbuye wakeyo anakwiya,+ ndipo anamupereka kwa oyang’anira ndende, mpaka pamene adzabweze ngongole yonse. Yakobo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti wosachita chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo n’chopambana kwambiri kuposa chiweruzo.
34 Pamenepo mbuye wakeyo anakwiya,+ ndipo anamupereka kwa oyang’anira ndende, mpaka pamene adzabweze ngongole yonse.
13 Pakuti wosachita chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo n’chopambana kwambiri kuposa chiweruzo.