Maliko 4:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Koma iwo anagwidwa mantha aakulu, ndipo anayamba kufunsana kuti: “Kodi ameneyu ndani kwenikweni, chifukwa ngakhale mphepo ndi nyanja zikumumvera?”+
41 Koma iwo anagwidwa mantha aakulu, ndipo anayamba kufunsana kuti: “Kodi ameneyu ndani kwenikweni, chifukwa ngakhale mphepo ndi nyanja zikumumvera?”+