Maliko 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma masiku adzafika pamene mkwatiyo adzachotsedwa pakati pawo, ndipo pa tsiku limenelo adzasala kudya.+ Luka 5:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Koma masiku adzafika pamene mkwati+ adzachotsedwa pakati pawo.+ Pamenepo iwo adzasala kudya masiku amenewo.”+
20 Koma masiku adzafika pamene mkwatiyo adzachotsedwa pakati pawo, ndipo pa tsiku limenelo adzasala kudya.+
35 Koma masiku adzafika pamene mkwati+ adzachotsedwa pakati pawo.+ Pamenepo iwo adzasala kudya masiku amenewo.”+