Yohane 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Tomasi, wotchedwa Didimo, anauza ophunzira anzakewo kuti: “Ifenso tiyeni tipite, kuti tikafere naye limodzi.”+ Yohane 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako anauza Tomasi kuti: “Ika chala chako apa, ndiponso ona m’manja mwangamu. Gwiranso ndi dzanja lako+ m’mbali mwa mimba yangamu, kuti usakhalenso wosakhulupirira, koma wokhulupirira.”
16 Choncho Tomasi, wotchedwa Didimo, anauza ophunzira anzakewo kuti: “Ifenso tiyeni tipite, kuti tikafere naye limodzi.”+
27 Kenako anauza Tomasi kuti: “Ika chala chako apa, ndiponso ona m’manja mwangamu. Gwiranso ndi dzanja lako+ m’mbali mwa mimba yangamu, kuti usakhalenso wosakhulupirira, koma wokhulupirira.”