Genesis 38:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma mwanayo anabweza dzanja lake. Nthawi yomweyo m’bale wake anatuluka, moti mzambayo anafuula kuti: “Ndiye chiyani wachitachi? Bwanji ukuchita kung’amba wekha njira?” N’chifukwa chake anamutcha dzina lakuti Perezi.*+ 1 Mbiri 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamara+ mpongozi wake ndiye anam’berekera Perezi+ ndi Zera. Ana onse a Yuda anali asanu.
29 Koma mwanayo anabweza dzanja lake. Nthawi yomweyo m’bale wake anatuluka, moti mzambayo anafuula kuti: “Ndiye chiyani wachitachi? Bwanji ukuchita kung’amba wekha njira?” N’chifukwa chake anamutcha dzina lakuti Perezi.*+