Mateyu 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atafika kumeneko anakakhala mumzinda wotchedwa Nazareti+ kuti akwaniritsidwe mawu onenedwa kudzera mwa aneneri kuti: “Iye adzatchedwa Mnazareti.”+ Maliko 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako anachoka kumeneko ndi kufika m’dera lakwawo, ndipo ophunzira ake anam’tsatira.+
23 Atafika kumeneko anakakhala mumzinda wotchedwa Nazareti+ kuti akwaniritsidwe mawu onenedwa kudzera mwa aneneri kuti: “Iye adzatchedwa Mnazareti.”+