Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Amene akutsogolera anthuwa ndiwo amene akuwasocheretsa,+ ndipo amene akutsogoleredwawo ndiwo amene akusokonezedwa.+

  • Malaki 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Koma inu mwapatuka panjira yoyenera.+ Mwalepheretsa anthu ambiri kutsatira chilamulo.+ Mwaphwanya pangano limene ndinapangana ndi Levi,”+ watero Yehova wa makamu.

  • Mateyu 23:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Tsoka kwa inu atsogoleri akhungu,+ amene mumati, ‘Ngati munthu walumbirira kachisi palibe kanthu, koma ngati munthu walumbirira golide wa m’kachisi, asunge lumbiro lake.’+

  • Luka 6:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Kenako anawauzanso fanizo lakuti: “Wakhungu sangatsogolere wakhungu mnzake, angatero ngati? Ngati atatero onse awiri angagwere m’dzenje, si choncho kodi?+

  • Yohane 9:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Afarisi amene anali naye anamva zimenezi, ndipo anafunsa Yesu kuti: “Kodi ifenso tingakhale akhungu?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena