Maliko 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho onse okhala m’dera la Yudeya ndi onse okhala mu Yerusalemu anakhamukira kwa iye. Chotero iye anawabatiza mumtsinje wa Yorodano ndipo anthuwo anali kuulula machimo awo poyera.+ Maliko 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 M’masiku amenewo, Yesu anabwera kuchokera ku Nazareti wa ku Galileya ndipo anabatizidwa ndi Yohane mu Yorodano.+
5 Choncho onse okhala m’dera la Yudeya ndi onse okhala mu Yerusalemu anakhamukira kwa iye. Chotero iye anawabatiza mumtsinje wa Yorodano ndipo anthuwo anali kuulula machimo awo poyera.+
9 M’masiku amenewo, Yesu anabwera kuchokera ku Nazareti wa ku Galileya ndipo anabatizidwa ndi Yohane mu Yorodano.+