Mateyu 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mtengo uliwonse wosabala zipatso zabwino amaudula ndi kuuponya pamoto.+ Luka 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako anayamba kufotokoza fanizo ili: “Munthu wina anali ndi mkuyu m’munda wake wa mpesa,+ ndipo anapita kukafuna chipatso mumtengowo,+ koma sanapezemo chilichonse.+
6 Kenako anayamba kufotokoza fanizo ili: “Munthu wina anali ndi mkuyu m’munda wake wa mpesa,+ ndipo anapita kukafuna chipatso mumtengowo,+ koma sanapezemo chilichonse.+