Machitidwe 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mpulumutsi+ ameneyu asanafike, Yohane+ anali atalalikiriratu poyera kwa anthu onse mu Isiraeli za ubatizo, monga chizindikiro cha kulapa. Machitidwe 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Paulo anati: “Yohane anabatiza anthu ubatizo umene unali chizindikiro chakuti munthu walapa.+ Anali kuuza anthu kuti akhulupirire amene anali kubwera m’mbuyo mwake,+ kutanthauza Yesu.”
24 Mpulumutsi+ ameneyu asanafike, Yohane+ anali atalalikiriratu poyera kwa anthu onse mu Isiraeli za ubatizo, monga chizindikiro cha kulapa.
4 Pamenepo Paulo anati: “Yohane anabatiza anthu ubatizo umene unali chizindikiro chakuti munthu walapa.+ Anali kuuza anthu kuti akhulupirire amene anali kubwera m’mbuyo mwake,+ kutanthauza Yesu.”