22 Zimene zafesedwa paminga, ndi munthu amene amamva mawu, koma nkhawa za moyo wa m’nthawi* ino+ ndiponso chinyengo champhamvu cha chuma zimalepheretsa mawuwo kukula, ndipo iye amakhala wosabala zipatso.+
14 Zimene zinagwera paminga, ndi anthu amene amva mawu a Mulungu. Koma chifukwa chotengeka ndi nkhawa, chuma ndi zosangalatsa za moyo uno,+ amalephera kukula bwino, ndipo zipatso zawo sizikhwima.+