Luka 11:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma Mfarisiyo anadabwa kuona kuti anayamba kudya chakudyacho asanasambe.+