-
Mateyu 15:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Koma inu mumanena kuti, ‘Aliyense wouza bambo ake kapena mayi ake kuti: “Chilichonse chimene ine ndili nacho, chimene ndikanakuthandizirani, ndi mphatso yoperekedwa kwa Mulungu,”
-
-
Mateyu 23:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Komanso mumati, ‘Ngati munthu walumbirira guwa lansembe, palibe kanthu, koma ngati munthu walumbirira mphatso imene ili paguwapo, asunge lumbiro lake.’
-