Mateyu 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Petulo anam’pempha kuti: “Timasulireni fanizo lija.”+ Luka 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma ophunzira ake anayamba kumufunsa tanthauzo la fanizo limeneli.+