Mateyu 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno kunabwera mayi wina wa ku Foinike+ kuchokera m’zigawo zimenezo ndi kufuula kuti: “Ndichitireni chifundo+ Ambuye, Mwana wa Davide. Mwana wanga wamkazi wagwidwa ndi chiwanda mochititsa mantha.”
22 Ndiyeno kunabwera mayi wina wa ku Foinike+ kuchokera m’zigawo zimenezo ndi kufuula kuti: “Ndichitireni chifundo+ Ambuye, Mwana wa Davide. Mwana wanga wamkazi wagwidwa ndi chiwanda mochititsa mantha.”