Mateyu 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Patapita masiku 6 Yesu anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane m’bale wake, n’kukwera nawo m’phiri lalitali kwaokhaokha.+ Luka 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Patapita masiku pafupifupi 8 chinenereni mawu amenewa, iye anatenga Petulo, Yohane ndi Yakobo ndi kukwera nawo m’phiri kukapemphera.+
17 Patapita masiku 6 Yesu anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane m’bale wake, n’kukwera nawo m’phiri lalitali kwaokhaokha.+
28 Patapita masiku pafupifupi 8 chinenereni mawu amenewa, iye anatenga Petulo, Yohane ndi Yakobo ndi kukwera nawo m’phiri kukapemphera.+