Mateyu 26:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa chomva chisoni kwambiri ndi zimenezi, aliyense anayamba kumufunsa kuti: “Ambuye, kodi ndine kapena?”+ Luka 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho anayamba kufunsana ndi kukambirana pakati pawo za amene anakonza chiwembu chimenecho.+ Yohane 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ophunzirawo anayamba kuyang’anizana posadziwa kuti anali kunena ndani.+
22 Chifukwa chomva chisoni kwambiri ndi zimenezi, aliyense anayamba kumufunsa kuti: “Ambuye, kodi ndine kapena?”+