Mateyu 26:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Popita kumeneko anatenga Petulo ndi ana awiri+ a Zebedayo. Ndipo anayamba kumva chisoni ndi kuvutika kwambiri mumtima mwake.+
37 Popita kumeneko anatenga Petulo ndi ana awiri+ a Zebedayo. Ndipo anayamba kumva chisoni ndi kuvutika kwambiri mumtima mwake.+