Aroma 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Popeza simunalandire mzimu wa ukapolo woyambitsanso mantha,+ koma munalandira mzimu+ wakuti mukhale ana,+ umene timafuula nawo kuti: “Abba,*+ Atate!” Agalatiya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano pakuti ndinu ana ake, Mulunguyo watitumizira mzimu+ wa Mwana wake m’mitima yathu ndipo mzimuwo ukufuula kuti: “Abba,* Atate!”+
15 Popeza simunalandire mzimu wa ukapolo woyambitsanso mantha,+ koma munalandira mzimu+ wakuti mukhale ana,+ umene timafuula nawo kuti: “Abba,*+ Atate!”
6 Tsopano pakuti ndinu ana ake, Mulunguyo watitumizira mzimu+ wa Mwana wake m’mitima yathu ndipo mzimuwo ukufuula kuti: “Abba,* Atate!”+