Mateyu 26:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 ndi kunena kuti: “Munthu ameneyu ananena kuti, ‘Ndikhoza kugwetsa kachisi wa Mulungu ndi kumumanganso m’masiku atatu.’”+ Maliko 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Anthu amene anali kudutsa pamenepo anali kumulankhula monyoza.+ Anali kupukusa mitu yawo n’kumanena kuti: “Iwe wogwetsa kachisi ndi kum’manga m’masiku atatu,+ Yohane 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yesu anawayankha kuti: “Gwetsani kachisi uyu,+ ndipo ine ndidzamumanga m’masiku atatu.”
61 ndi kunena kuti: “Munthu ameneyu ananena kuti, ‘Ndikhoza kugwetsa kachisi wa Mulungu ndi kumumanganso m’masiku atatu.’”+
29 Anthu amene anali kudutsa pamenepo anali kumulankhula monyoza.+ Anali kupukusa mitu yawo n’kumanena kuti: “Iwe wogwetsa kachisi ndi kum’manga m’masiku atatu,+