Mateyu 27:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo pa nthawiyi panali mkaidi wina wowopsa kwambiri wotchedwa Baraba.+