Mateyu 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma mngeloyo+ anauza amayiwo kuti: “Inu musachite mantha, chifukwa ndikudziwa kuti mukufuna Yesu+ amene anapachikidwa. Luka 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Atathedwa nzeru ndi zimenezi, anangoona amuna awiri ovala zovala zonyezimira ataima pambali pawo.+
5 Koma mngeloyo+ anauza amayiwo kuti: “Inu musachite mantha, chifukwa ndikudziwa kuti mukufuna Yesu+ amene anapachikidwa.