Mateyu 5:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense wothetsa ukwati ndi mkazi wake, osati chifukwa cha dama,*+ amamuchititsa chigololo akakwatiwanso,+ ndipo aliyense wokwatira mkazi wosiyidwayo nayenso wachita chigololo.+ Mateyu 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ine ndikukuuzani kuti aliyense wosiya mkazi wake n’kukwatira wina wachita chigololo, kupatulapo ngati wamusiya chifukwa cha dama.”*+ Maliko 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anawauza kuti: “Aliyense wosiya mkazi wake ndi kukwatira wina, wachita chigololo+ molakwira mkaziyo.
32 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense wothetsa ukwati ndi mkazi wake, osati chifukwa cha dama,*+ amamuchititsa chigololo akakwatiwanso,+ ndipo aliyense wokwatira mkazi wosiyidwayo nayenso wachita chigololo.+
9 Ine ndikukuuzani kuti aliyense wosiya mkazi wake n’kukwatira wina wachita chigololo, kupatulapo ngati wamusiya chifukwa cha dama.”*+
11 Iye anawauza kuti: “Aliyense wosiya mkazi wake ndi kukwatira wina, wachita chigololo+ molakwira mkaziyo.