Miyambo 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kudzudzula kumam’fika pamtima munthu womvetsa zinthu,+ kuposa kukwapula munthu wopusa zikwapu 100.+ Maliko 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pamenepo Yesu anatembenuka, ndi kuyang’ana ophunzira ake, kenako anakalipira Petulo kuti: “Pita kumbuyo kwanga Satana, chifukwa zimene umaganiza si maganizo a Mulungu, koma maganizo a anthu.”+
10 Kudzudzula kumam’fika pamtima munthu womvetsa zinthu,+ kuposa kukwapula munthu wopusa zikwapu 100.+
33 Pamenepo Yesu anatembenuka, ndi kuyang’ana ophunzira ake, kenako anakalipira Petulo kuti: “Pita kumbuyo kwanga Satana, chifukwa zimene umaganiza si maganizo a Mulungu, koma maganizo a anthu.”+