Luka 9:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamene masiku oti akwere kumwamba+ anali kukwana, anatsimikiza mtima kupita ku Yerusalemu. Yohane 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma anafunika kuti adzere ku Samariya.+