Levitiko 13:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Masiku onse pamene akudwala nthendayo azikhala wodetsedwa. Iye ndi wodetsedwa ndipo azikhala payekha. Azikhala kunja kwa msasa.+ Mateyu 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako panafika munthu wakhate.+ Munthuyo anamugwadira n’kunena kuti: “Ambuye, ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”
46 Masiku onse pamene akudwala nthendayo azikhala wodetsedwa. Iye ndi wodetsedwa ndipo azikhala payekha. Azikhala kunja kwa msasa.+
2 Kenako panafika munthu wakhate.+ Munthuyo anamugwadira n’kunena kuti: “Ambuye, ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”