Mateyu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yesu anatembenuka, ndipo anaona mayiyo n’kunena kuti: “Mwanawe, limba mtima, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+ Kuchokera pa ola limenelo mayiyo anachira.+ Maliko 5:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iye anauza mayiyo kuti: “Mwanawe, chikhulupiriro chako chakuchiritsa. Pita mu mtendere,+ matenda ako aakuluwo atheretu.”+ Luka 7:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Koma iye anauza mayiyo kuti: “Chikhulupiriro chako chakupulumutsa.+ Pita mu mtendere.”+
22 Yesu anatembenuka, ndipo anaona mayiyo n’kunena kuti: “Mwanawe, limba mtima, chikhulupiriro chako chakuchiritsa.”+ Kuchokera pa ola limenelo mayiyo anachira.+
34 Iye anauza mayiyo kuti: “Mwanawe, chikhulupiriro chako chakuchiritsa. Pita mu mtendere,+ matenda ako aakuluwo atheretu.”+