Mateyu 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Chotero munthu akadzakuuzani kuti, ‘Onani! Khristu uja ali kuno,’+ kapena, ‘Ali uko!’ musadzakhulupirire zimenezo.+ Maliko 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Komanso pa nthawiyo, munthu akadzakuuzani kuti, ‘Onani! Khristu uja ali kuno,’+ ‘Onani! Ali uko,’ musadzakhulupirire zimenezo.+
23 “Chotero munthu akadzakuuzani kuti, ‘Onani! Khristu uja ali kuno,’+ kapena, ‘Ali uko!’ musadzakhulupirire zimenezo.+
21 “Komanso pa nthawiyo, munthu akadzakuuzani kuti, ‘Onani! Khristu uja ali kuno,’+ ‘Onani! Ali uko,’ musadzakhulupirire zimenezo.+