Mateyu 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Chotero munthu akadzakuuzani kuti, ‘Onani! Khristu uja ali kuno,’+ kapena, ‘Ali uko!’ musadzakhulupirire zimenezo.+ Maliko 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Komanso pa nthawiyo, munthu akadzakuuzani kuti, ‘Onani! Khristu uja ali kuno,’+ ‘Onani! Ali uko,’ musadzakhulupirire zimenezo.+ Luka 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anayankha kuti: “Samalani kuti asadzakusocheretseni.+ Pakuti ambiri adzabwera m’dzina langa, n’kumanena kuti, ‘Khristu uja ndine,’ adzanenanso kuti, ‘Nthawi ija yayandikira.’+ Musadzawatsatire.
23 “Chotero munthu akadzakuuzani kuti, ‘Onani! Khristu uja ali kuno,’+ kapena, ‘Ali uko!’ musadzakhulupirire zimenezo.+
21 “Komanso pa nthawiyo, munthu akadzakuuzani kuti, ‘Onani! Khristu uja ali kuno,’+ ‘Onani! Ali uko,’ musadzakhulupirire zimenezo.+
8 Iye anayankha kuti: “Samalani kuti asadzakusocheretseni.+ Pakuti ambiri adzabwera m’dzina langa, n’kumanena kuti, ‘Khristu uja ndine,’ adzanenanso kuti, ‘Nthawi ija yayandikira.’+ Musadzawatsatire.