Genesis 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komabe, m’kachizirezire ka m’bandakucha, angelowo anayamba kum’fulumiza Loti, kuti: “Fulumira! Tenga mkazi wako ndi ana ako aakazi awiriwa,+ kuti musawonongedwere limodzi ndi mzindawu chifukwa cha kulakwa kwake.”+
15 Komabe, m’kachizirezire ka m’bandakucha, angelowo anayamba kum’fulumiza Loti, kuti: “Fulumira! Tenga mkazi wako ndi ana ako aakazi awiriwa,+ kuti musawonongedwere limodzi ndi mzindawu chifukwa cha kulakwa kwake.”+