Genesis 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Yehova anavumbitsa sulufule ndi moto kuchokera kwa Yehova kumwamba, kuvumbira pa Sodomu ndi Gomora.+
24 Ndiyeno Yehova anavumbitsa sulufule ndi moto kuchokera kwa Yehova kumwamba, kuvumbira pa Sodomu ndi Gomora.+