Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 10:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Aliyense wopulumutsa moyo wake adzautaya, ndipo wotaya moyo wake chifukwa cha ine adzaupeza.+

  • Mateyu 16:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pakuti aliyense wofuna kupulumutsa moyo wake adzautaya, koma aliyense wotaya moyo wake chifukwa cha ine adzaupeza.+

  • Maliko 8:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Pakuti aliyense wofuna kupulumutsa moyo wake adzautaya. Koma aliyense wotaya moyo wake chifukwa cha ine ndi uthenga wabwino, adzaupulumutsa.+

  • Luka 9:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pakuti aliyense wofuna kupulumutsa moyo wake adzautaya. Koma aliyense wotaya moyo wake chifukwa cha ine, adzaupulumutsa.+

  • Yohane 12:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Aliyense wokonda moyo wake akuuwononga, koma wodana ndi moyo wake+ m’dziko lino akuusungira moyo wosatha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena