Miyambo 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pali m’badwo umene umadziona kuti ndi woyera,+ koma sunasambe kuti uchotse ndowe zake.+ Luka 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma pofuna kudzionetsa kuti ndi wolungama, munthuyo anafunsa Yesu kuti: “Nanga mnzanga amene ndikuyenera kumukonda ndani kwenikweni?”+
29 Koma pofuna kudzionetsa kuti ndi wolungama, munthuyo anafunsa Yesu kuti: “Nanga mnzanga amene ndikuyenera kumukonda ndani kwenikweni?”+