Miyambo 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Wodalira chuma chake adzagwa,+ koma anthu olungama adzasangalala ngati masamba a zomera.+ Mateyu 19:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Ndithu ndikukuuzani, zidzakhalatu zovuta kuti munthu wolemera adzalowe mu ufumu wakumwamba.+ 1 Timoteyo 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komabe, anthu ofunitsitsa kulemera, amagwera m’mayesero+ ndi mumsampha. Iwo amakodwa ndi zilakolako zambiri zowapweteketsa ndiponso amachita zinthu mopanda nzeru.+ Zinthu zimenezi zimawawononga ndi kuwabweretsera mavuto.+
23 Koma Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Ndithu ndikukuuzani, zidzakhalatu zovuta kuti munthu wolemera adzalowe mu ufumu wakumwamba.+
9 Komabe, anthu ofunitsitsa kulemera, amagwera m’mayesero+ ndi mumsampha. Iwo amakodwa ndi zilakolako zambiri zowapweteketsa ndiponso amachita zinthu mopanda nzeru.+ Zinthu zimenezi zimawawononga ndi kuwabweretsera mavuto.+