Genesis 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pambuyo pake Yehova anauza Nowa kuti: “Lowa m’chingalawacho, iwe ndi banja lako,+ chifukwa iwe ndi amene ndakuona kuti ndiwe wolungama pakati pa m’badwo uwu.+ Afilipi 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kunena za kudzipereka, ndinali kuzunza mpingo.+ Kunena za chilungamo mwa kutsatira chilamulo, ndinakhaladi wopanda chifukwa chondinenezera.
7 Pambuyo pake Yehova anauza Nowa kuti: “Lowa m’chingalawacho, iwe ndi banja lako,+ chifukwa iwe ndi amene ndakuona kuti ndiwe wolungama pakati pa m’badwo uwu.+
6 Kunena za kudzipereka, ndinali kuzunza mpingo.+ Kunena za chilungamo mwa kutsatira chilamulo, ndinakhaladi wopanda chifukwa chondinenezera.