Mateyu 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsopano pamene iwo anali kutuluka mu Yeriko,+ khamu lalikulu la anthu linam’tsatira.