Mateyu 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma poona zimenezi, Afarisi anayamba kufunsa ophunzira ake kuti: “N’chifukwa chiyani mphunzitsi wanu amadya limodzi ndi okhometsa msonkho ndi anthu ochimwa?”+ Luka 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Afarisi ndi alembi awo ataona izi, anayamba kung’ung’udza ndi kufunsa ophunzira ake kuti: “N’chifukwa chiyani inu mumadya ndi kumwa limodzi ndi okhometsa msonkho ndi anthu ochimwa?”+ Luka 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Afarisi ndi alembi ataona zimenezi anayamba kung’ung’udza kuti: “Munthu uyu amalandira anthu ochimwa ndi kudya nawo limodzi.”+
11 Koma poona zimenezi, Afarisi anayamba kufunsa ophunzira ake kuti: “N’chifukwa chiyani mphunzitsi wanu amadya limodzi ndi okhometsa msonkho ndi anthu ochimwa?”+
30 Afarisi ndi alembi awo ataona izi, anayamba kung’ung’udza ndi kufunsa ophunzira ake kuti: “N’chifukwa chiyani inu mumadya ndi kumwa limodzi ndi okhometsa msonkho ndi anthu ochimwa?”+
2 Afarisi ndi alembi ataona zimenezi anayamba kung’ung’udza kuti: “Munthu uyu amalandira anthu ochimwa ndi kudya nawo limodzi.”+