Mateyu 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Poyankha iye anati: “Ine sananditumize kwa wina aliyense koma kwa nkhosa zotayika za nyumba ya Isiraeli.”+ Luka 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi sikunali koyenera kuti mayi uyu, amenenso ndi mwana wa Abulahamu,+ amene Satana anamumanga zaka 18, amasulidwe m’maunyolo amenewa tsiku la sabata?” Machitidwe 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Inu ndinu ana+ a aneneri ndi a pangano limene Mulungu anapangana ndi makolo anu akale. Iye anauza Abulahamu kuti, ‘Kudzera mwa mbewu yako mabanja onse a padziko lapansi adzadalitsidwa.’+
24 Poyankha iye anati: “Ine sananditumize kwa wina aliyense koma kwa nkhosa zotayika za nyumba ya Isiraeli.”+
16 Kodi sikunali koyenera kuti mayi uyu, amenenso ndi mwana wa Abulahamu,+ amene Satana anamumanga zaka 18, amasulidwe m’maunyolo amenewa tsiku la sabata?”
25 Inu ndinu ana+ a aneneri ndi a pangano limene Mulungu anapangana ndi makolo anu akale. Iye anauza Abulahamu kuti, ‘Kudzera mwa mbewu yako mabanja onse a padziko lapansi adzadalitsidwa.’+