Mateyu 25:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako kunabwera kapolo amene analandira matalente awiri uja n’kunena kuti, ‘Ambuye, paja munandipatsa matalente awiri koma onani, ndapindula matalente enanso awiri.’+
22 Kenako kunabwera kapolo amene analandira matalente awiri uja n’kunena kuti, ‘Ambuye, paja munandipatsa matalente awiri koma onani, ndapindula matalente enanso awiri.’+