Mateyu 25:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mbuye wake anamuyankha kuti, ‘Wachita bwino kwambiri, kapolo wabwino ndi wokhulupirika iwe! Unakhulupirika pa zinthu zochepa. Ndikuika kuti uziyang’anira zinthu zambiri.+ Sangalala+ limodzi ndi ine mbuye wako.’
23 Mbuye wake anamuyankha kuti, ‘Wachita bwino kwambiri, kapolo wabwino ndi wokhulupirika iwe! Unakhulupirika pa zinthu zochepa. Ndikuika kuti uziyang’anira zinthu zambiri.+ Sangalala+ limodzi ndi ine mbuye wako.’