Mateyu 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yakobo anabereka Yosefe mwamuna wake wa Mariya, amene anabereka Yesu,+ wotchedwa Khristu.+