Mateyu 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 n’kuwauza kuti: “Pitani m’mudzi umene mukuuonawo. Kumeneko mukapeza bulu atam’mangirira limodzi ndi mwana wake wamphongo. Mukawamasule ndi kuwabweretsa kwa ine.+ Maliko 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndi kuwauza kuti: “Pitani m’mudzi umene mukuuonawo. Mukakalowa mmenemo, mukapeza bulu wamng’ono wamphongo atam’mangirira, amene munthu sanakwerepo chiyambire. Mukam’masule ndi kubwera naye kuno.+
2 n’kuwauza kuti: “Pitani m’mudzi umene mukuuonawo. Kumeneko mukapeza bulu atam’mangirira limodzi ndi mwana wake wamphongo. Mukawamasule ndi kuwabweretsa kwa ine.+
2 ndi kuwauza kuti: “Pitani m’mudzi umene mukuuonawo. Mukakalowa mmenemo, mukapeza bulu wamng’ono wamphongo atam’mangirira, amene munthu sanakwerepo chiyambire. Mukam’masule ndi kubwera naye kuno.+