Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 50:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti nyama iliyonse yakutchire ndi yanga,+

      Ndiponso nyama zopezeka m’mapiri 1,000.+

  • Mateyu 21:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Wina aliyense akakakufunsani chilichonse, mukanene kuti, ‘Ambuye akuwafuna.’ Ndipo nthawi yomweyo akawatumiza kuno.”

  • Maliko 11:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Wina akakakufunsani kuti, ‘N’chifukwa chiyani mukumumasula?’ Mukanene kuti, ‘Ambuye akumufuna, ndipo akangotha kum’gwiritsa ntchito am’bweza nthawi yomweyo.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena